1 Mbiri 7:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo anayesedwa mwa chibadwidwe chao, mwa mibadwo yao, akulu a nyumba za makolo ao, ngwazi zamphamvu zikwi makumi awiri mphambu mazana awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo anayesedwa mwa chibadwidwe chao, mwa mibadwo yao, akulu a nyumba za makolo ao, ngwazi zamphamvu zikwi makumi awiri mphambu mazana awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ndipo kulembedwa kwao potsata kubadwa kwao ndiponso malinga ndi mibadwo yao, pokhala atsogoleri a mabanja a makolo ao, analipo 20,200, ankhondo amphamvu okhaokha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Pa mndandanda wa mʼbado wawo panali atsogoleri a mabanja ndi anthu 20,200 odziwa kumenya nkhondo. Onani mutuwo |