Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 7:8 - Buku Lopatulika

8 Ndi ana a Bekere: Zimira, ndi Yowasi, ndi Eliyezere, ndi Eliyoenai, ndi Omuri, ndi Yeremoti, ndi Abiya, ndi Anatoti, ndi Alemeti. Onsewa ndiwo ana a Bekere.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndi ana a Bekere: Zimira, ndi Yowasi, ndi Eliyezere, ndi Eliyoenai, ndi Omuri, ndi Yeremoti, ndi Abiya, ndi Anatoti, ndi Alemeti. Onsewa ndiwo ana a Bekere.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Ana a Bekere naŵa: Zimira, Yowasi, Eliyezere, Eliyoenai, Omuri, Yeremoti, Abiya, Anatoti ndi Alemeti. Onseŵa anali ana a Bekere.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Ana a Bekeri anali awa: Zemira, Yowasi, Eliezara, Eliyoenai, Omiri, Yeremoti, Abiya, Anatoti ndi Alemeti. Onsewa anali ana a Bekeri.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 7:8
3 Mawu Ofanana  

Ndi ana aamuna a Benjamini: Bela ndi Bekere, ndi Asibele, ndi Gera, ndi Naamani, ndi Ehi ndi Rosi, Mupimu ndi Hupimu, ndi Aridi.


Ndi ana a Bela: Eziboni, ndi Uzi, ndi Uziyele, ndi Yerimoti, ndi Iri, asanu; akulu a nyumba za makolo ao, ngwazi zamphamvu, owerengedwa m'mabuku a chibadwidwe zikwi makumi awiri mphambu ziwiri kudza makumi atatu ndi anai.


Ndipo anayesedwa mwa chibadwidwe chao, mwa mibadwo yao, akulu a nyumba za makolo ao, ngwazi zamphamvu zikwi makumi awiri mphambu mazana awiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa