Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -

1 Mbiri 7:7 - Buku Lopatulika

7 Ndi ana a Bela: Eziboni, ndi Uzi, ndi Uziyele, ndi Yerimoti, ndi Iri, asanu; akulu a nyumba za makolo ao, ngwazi zamphamvu, owerengedwa m'mabuku a chibadwidwe zikwi makumi awiri mphambu ziwiri kudza makumi atatu ndi anai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ndi ana a Bela: Eziboni, ndi Uzi, ndi Uziyele, ndi Yerimoti, ndi Iri, asanu; akulu a nyumba za makolo ao, ngwazi zamphamvu, owerengedwa m'mabuku a chibadwidwe zikwi makumi awiri mphambu ziwiri kudza makumi atatu ndi anai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Ana a Bela naŵa: Eziboni, Uzi, Uziyele, Yerimoti ndi Iri, asanu, atsogoleri a mabanja a makolo ao, ankhondo amphamvu. Ndipo chiŵerengero chao potsata mibadwo yao chinali 22,034.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Ana a Bela anali awa: Eziboni, Uzi, Uzieli, Yerimoti ndi Iri. Iwowa anali atsogoleri a mabanja awo ndipo onse pamodzi analipo asanu. Pa mndandanda wa mʼbado wawo panali anthu 22,034 odziwa kumenya nkhondo.

Onani mutuwo Koperani

1 Mbiri 7:7
4 Mawu Ofanana  

Ana a Benjamini ndiwo Bela, ndi Bekere, ndi Yediyaele, atatu.

Ndi ana a Bekere: Zimira, ndi Yowasi, ndi Eliyezere, ndi Eliyoenai, ndi Omuri, ndi Yeremoti, ndi Abiya, ndi Anatoti, ndi Alemeti. Onsewa ndiwo ana a Bekere.

Titsatireni:

Zotsatsa

Zotsatsa