1 Mbiri 7:5 - Buku Lopatulika5 Ndi abale ao mwa mabanja onse a Isakara, ngwazi zamphamvu, oyesedwa mwa chibadwidwe chao, onsewa ndiwo zikwi zisanu ndi zitatu mphambu zisanu ndi ziwiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndi abale ao mwa mabanja onse a Isakara, ngwazi zamphamvu, oyesedwa mwa chibadwidwe chao, onsewa ndiwo zikwi zisanu ndi zitatu mphambu zisanu ndi ziwiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Abale ao a mabanja onse a Isakara analipo onse pamodzi 87,000, ankhondo amphamvu, olembedwa potsata mibadwo yao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Abale awo onse a mʼbanja la Isakara amene anali odziwa kumenya nkhondo analipo 87,000, olembedwa potsata mibado yawo. Onani mutuwo |