1 Mbiri 7:4 - Buku Lopatulika4 Ndi pamodzi nao mwa mibadwo yao, mwa nyumba za makolo ao, panali magulu a nkhondo zikwi makumi atatu mphambu zisanu ndi chimodzi, popeza anachuluka akazi ao ndi ana ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndi pamodzi nao mwa mibadwo yao, mwa nyumba za makolo ao, panali magulu a nkhondo zikwi makumi atatu mphambu zisanu ndi chimodzi, popeza anachuluka akazi ao ndi ana ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Pamodzi ndi iwowo, malinga ndi mibadwo yao ndi mabanja a makolo ao, panali anthu ankhondo 36,000, pakuti anali ndi akazi ambiri ndiponso ana ambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Monga mwa chiwerengero cha mabanja awo, panali anthu 36,000 odziwa kumenya nkhondo, pakuti iwo anali ndi akazi ndi ana ambiri. Onani mutuwo |