1 Mbiri 7:3 - Buku Lopatulika3 Ndi mwana wa Uzi: Izrahiya; ndi ana a Izrahiya: Mikaele, ndi Obadiya, ndi Yowele, ndi Isiya; onse asanuwa ndiwo akulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndi mwana wa Uzi: Izrahiya; ndi ana a Izrahiya: Mikaele, ndi Obadiya, ndi Yowele, ndi Isiya; onse asanuwa ndiwo akulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mwana wa Uzi anali Iziraya. Ana a Iziraya naŵa: Mikaele, Obadiya, Yowele ndiponso Isiya. Asanu onsewo anali atsogoleri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Mwana wa Uzi anali Izirahiya. Ana a Izirahiya anali: Mikayeli, Obadiya, Yoweli ndi Isiya. Onse asanu anali atsogoleri a mabanja. Onani mutuwo |