1 Mbiri 7:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo Refa anali mwana wake, ndi Resefi, ndi Tela mwana wake, ndi Tahani mwana wake, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo Refa anali mwana wake, ndi Resefi, ndi Tela mwana wake, ndi Tahani mwana wake, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Mwana wina wa Efuremu anali Refa, amene zidzukulu zake zinali izi: Resefi, Tela, Tahani, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Mwana wina wa Efereimu anali Refa amene zidzukulu zake zinali Resefu, Tela, Tahani, Onani mutuwo |