1 Mbiri 7:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo analowa kwa mkazi wake, naima iye, nabala mwana, namutcha dzina lake Beriya, popeza m'nyumba mwake mudaipa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo analowa kwa mkazi wake, naima iye, nabala mwana, namutcha dzina lake Beriya, popeza m'nyumba mwake mudaipa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Pambuyo pake Efuremu adakaloŵa kwa mkazi wake, ndipo mkaziyo adatenga pathupi nabala mwana. Mwanayo adamutcha dzina loti Beriya, chifukwa chakuti tsoka lidaagwera banja lake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Kenaka anagona ndi mkazi wake, ndipo anakhala woyembekezera nabala mwana wamwamuna. Anamutcha dzina lake Beriya, chifukwa tsoka linagwera banja lake. Onani mutuwo |