1 Mbiri 7:19 - Buku Lopatulika19 Ndi ana a Semida ndiwo Ahiyani, ndi Sekemu, ndi Liki, ndi Aniyamu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndi ana a Semida ndiwo Ahiyani, ndi Sekemu, ndi Liki, ndi Aniyamu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Ana a Semida naŵa: Ahiyani, Sekemu, Liki ndi Aniyamu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Ana a Semida anali: Ahiyani, Sekemu, Likihi ndi Aniyamu. Onani mutuwo |