Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 7:12 - Buku Lopatulika

12 Supimu yemwe ndi Hupimu ana a Iri, ndi Husimu mwana wa Aheri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Supimu yemwe ndi Hupimu ana a Iri, ndi Husimu mwana wa Aheri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Supimu ndi Hupimu anali ana a Iri, ndipo analinso a fuko ili. Husimu anali mwana wa Dan.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Asupi ndi Ahupi anali zidzukulu za Iri, ndipo Ahusimu anali zidzukulu za Aheri.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 7:12
7 Mawu Ofanana  

Ndi ana aamuna a Benjamini: Bela ndi Bekere, ndi Asibele, ndi Gera, ndi Naamani, ndi Ehi ndi Rosi, Mupimu ndi Hupimu, ndi Aridi.


Onsewa ndiwo ana a Yediyaele; ndiwo akulu a nyumba za makolo ao, ngwazi zamphamvu zikwi khumi mphambu zisanu ndi ziwiri kudza mazana awiri akutuluka kugulu kunkhondo.


Ana a Nafutali: Yaziyele, ndi Guni, ndi Yezere, ndi Salumu, ana a Biliha.


ndi Makiri anadzitengera mkazi, mlongo wake wa Hupimu ndi Supimu, dzina lake ndiye Maaka. Ndipo dzina la mwana wachiwiri wa Manase ndiye Zelofehadi. Ndi Zelofehadi anali ndi ana aakazi.


Ndipo Benjamini anabala Bela mwana wake woyamba, Asibele wachiwiri, ndi Ahara wachitatu,


ndi Gera, ndi Sefufani, ndi Huramu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa