1 Mbiri 7:11 - Buku Lopatulika11 Onsewa ndiwo ana a Yediyaele; ndiwo akulu a nyumba za makolo ao, ngwazi zamphamvu zikwi khumi mphambu zisanu ndi ziwiri kudza mazana awiri akutuluka kugulu kunkhondo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Onsewa ndiwo ana a Yediyaele; ndiwo akulu a nyumba za makolo ao, ngwazi zamphamvu zikwi khumi mphambu zisanu ndi ziwiri kudza mazana awiri akutuluka kugulu kunkhondo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Onseŵa anali ana a Yediyaele, atsogoleri a mabanja a makolo ao, ankhondo amphamvu 17,200, anthu okonzekera kumenya nkhondo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Ana onsewa a Yediaeli anali atsogoleri a mabanja. Analipo anthu 17,200 amene anali okonzeka kupita ku nkhondo. Onani mutuwo |