Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 7:10 - Buku Lopatulika

10 Ndi mwana wa Yediyaele: Bilihani; ndi ana a Bilihani: Yeusi, ndi Benjamini, ndi Ehudi, ndi Kenana, ndi Zetani, ndi Tarisisi, ndi Ahisahara.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndi mwana wa Yediyaele: Bilihani; ndi ana a Bilihani: Yeusi, ndi Benjamini, ndi Ehudi, ndi Kenana, ndi Zetani, ndi Tarisisi, ndi Ahisahara.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Mwana wa Yediyaele anali Bilihani. Ana a Bilihani naŵa: Yeusi, Benjamini, Ehudi, Kenana, Zetani, Tarisisi ndi Ahisahara.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Mwana wa Yediaeli anali Bilihani. Ana a Bilihani anali awa: Yeusi, Benjamini, Ehudi, Kenaana, Zetani, Tarisisi ndi Ahisahara.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 7:10
5 Mawu Ofanana  

Ndipo Zedekiya mwana wa Kenana anadzisulira nyanga zachitsulo, nati, Atero Yehova, Ndi izi mudzagunda nazo Aaramu mpaka atatha psiti.


Onsewa ndiwo ana a Yediyaele; ndiwo akulu a nyumba za makolo ao, ngwazi zamphamvu zikwi khumi mphambu zisanu ndi ziwiri kudza mazana awiri akutuluka kugulu kunkhondo.


Ndipo anayesedwa mwa chibadwidwe chao, mwa mibadwo yao, akulu a nyumba za makolo ao, ngwazi zamphamvu zikwi makumi awiri mphambu mazana awiri.


Ndi ana a Ehudi ndi awa: ndiwo akulu a nyumba za makolo ao a iwo okhala ku Geba, ndipo anawatenga ndende kunka ku Manahati,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa