1 Mbiri 6:2 - Buku Lopatulika2 Ndi ana a Kohati: Amuramu, Izihara, ndi Hebroni, ndi Uziyele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndi ana a Kohati: Amuramu, Izihara, ndi Hebroni, ndi Uziyele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Ana a Kohati naŵa: Amuramu, Izara, Hebroni ndi Uziyele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ana a Kohati anali awa: Amramu, Izihari, Hebroni ndi Uzieli. Onani mutuwo |