1 Mbiri 5:9 - Buku Lopatulika9 ndi kum'mawa anakhala mpaka polowera kuchipululu kuyambira mtsinje wa Yufurate; pakuti zoweta zao zinachuluka m'dziko la Giliyadi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 ndi kum'mawa anakhala mpaka polowera kuchipululu kuyambira mtsinje wa Yufurate; pakuti zoweta zao zinachuluka m'dziko la Giliyadi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Iwowo adakhala kuvuma mpaka kukafika poloŵera m'chipululu cha mbali ina ya Yufurate, chifukwa chakuti ng'ombe zao zinali zitaswana kwambiri m'dziko la Giliyadi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Iwo anakhala cha kummawa mpaka kukafika polowera mʼchipululu cha mbali ina ya Mtsinje wa Yufurate, chifukwa ziweto zawo zinaswana kwambiri mʼdziko la Giliyadi. Onani mutuwo |