1 Mbiri 5:7 - Buku Lopatulika7 Ndi abale ake monga mwa mabanja ao, powerenga chibadwidwe cha mibadwo yao: akulu ndiwo Yeiyele, ndi Zekariya, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndi abale ake monga mwa mabanja ao, powerenga chibadwidwe cha mibadwo yao: akulu ndiwo Yeiyele, ndi Zekariya, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Akuluakulu a fuko la Rubeni, potsata mndandanda wa maina ao, naŵa: mtsogoleri Yeiyele, Zekariya, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Abale awo mwa mabanja awo, potsata mndandanda wa mʼbado wawo, ndi awa: Yeiyeli, mtsogoleri, Zekariya, Onani mutuwo |