Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 5:16 - Buku Lopatulika

16 Ndipo anakhala mu Giliyadi mu Basani, ndi m'midzi yake, ndi podyetsa pake ponse pa Saroni, mpaka malire ao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Ndipo anakhala m'Giliyadi m'Basani, ndi m'midzi yake, ndi podyetsa pake ponse pa Saroni, mpaka malire ao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Iwowo adakhala m'midzi ya ku Giliyadi ndi ku Basani ndiponso ku mabusa onse a m'maiko a Saroni mpaka ku mapeto ake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Fuko la Gadi linakhala ku Giliyadi, ku Basani ndi midzi yozugulira, madera onse a msipu a ku Saroni mpaka kumene amalekezera.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 5:16
8 Mawu Ofanana  

ndi woyang'anira ng'ombe zakudya mu Saroni ndiye Sitirai Msaroni; ndi woyang'anira ng'ombe za m'zigwa ndiye Safati mwana wa Adilai;


Ahi mwana wa Abidiyele, mwana wa Guni, ndiye mkulu wa nyumba za makolo ao.


Ndine duwa lofiira la ku Saroni, ngakhale kakombo wa kuzigwa.


Lidzaphuka mochuluka ndi kusangalala, ngakhale kukondwa ndi kuimba; lidzapatsidwa ulemerero wa Lebanoni, ndi ukulu wa Karimele ndi Saroni; anthuwo adzaona ulemerero wa Yehova, ukulu wake wa Mulungu wathu.


Ndipo Saroni adzakhala podyetsera nkhosa, ndi chigwa cha Akori chidzakhala pogona zoweta kwa anthu anga amene andifuna Ine.


Ndipo anamuona iye onse akukhala ku Lida ndi ku Saroni, natembenukira kwa Ambuye amenewa.


Ndipo Mose anapatsira fuko la Gadi, ana a Gadi, monga mwa mabanja ao.


Ichi ndi cholowa cha ana a Gadi, monga mwa mabanja ao, mizinda yake ndi midzi yake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa