1 Mbiri 5:13 - Buku Lopatulika13 ndi abale ao a nyumba za makolo ao: Mikaele, ndi Mesulamu, ndi Sheba, ndi Yorai, ndi Yakani, ndi Ziya, ndi Eberi; asanu ndi awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 ndi abale ao a nyumba za makolo ao: Mikaele, ndi Mesulamu, ndi Sheba, ndi Yorai, ndi Yakani, ndi Ziya, ndi Eberi; asanu ndi awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Abale ao, potsata mabanja a makolo ao, naŵa: Mikaele, Mesulamu, Sheba, Yorai, Yakani, Ziya ndiponso Eberi, asanu ndi aŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Abale awo mwa mabanja awo anali awa: Mikayeli, Mesulamu, Seba, Yorayi, Yakani, Ziya ndi Eberi, onse ali asanu ndi awiri. Onani mutuwo |