1 Mbiri 5:12 - Buku Lopatulika12 Yowele mkulu wao, ndi Safamu wachiwiri, ndi Yanai, ndi Safati mu Basani; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Yowele mkulu wao, ndi Safamu wachiwiri, ndi Yanai, ndi Safati m'Basani; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Mkulu wao anali Yowele, ndipo wachiŵiri wake anali Safani. Panalinso Yanai, ndi Safati ku Basani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Mtsogoleri wawo ku Basani anali Yoweli, wachiwiri anali Safamu, kenaka Yanayi ndi Safati. Onani mutuwo |