Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 5:11 - Buku Lopatulika

11 Ndi ana a Gadi anakhala pandunji pao m'dziko la Basani mpaka Saleka:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndi ana a Gadi anakhala pandunji pao m'dziko la Basani mpaka Saleka:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Ana a Gadi adakhala kumpoto kwa Arubeni m'dziko la Basani mpaka kukafika ndithu kuvuma ku Saleka.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Anthu a fuko la Gadi anakhala moyandikana ndi fuko la Rubeni ku Basani mpaka ku Saleka:

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 5:11
7 Mawu Ofanana  

Yowele mkulu wao, ndi Safamu wachiwiri, ndi Yanai, ndi Safati mu Basani;


Ana aamuna a Gadi monga mwa mabanja ao ndiwo: Zefoni, ndiye kholo la banja la Azefoni; Hagi, ndiye kholo la banja la Ahagi; Suni, ndiye kholo la banja la Suni;


nachita ufumu m'phiri la Heremoni, ndi mu Saleka, ndi mu Basani lonse, mpaka malire a Agesuri, ndi a Maakati, ndi Giliyadi wogawika pakati, malire a Sihoni mfumu ya ku Hesiboni.


ndi Giliyadi, ndi malire a Agesuri, ndi Amaakati, ndi phiri lonse la Heremoni, ndi Basani lonse mpaka ku Saleka;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa