1 Mbiri 4:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo Yabezi analemekezedwa koposa abale ake; ndi make anamutcha dzina lake Yabezi, ndi kuti, Popeza ndambala mwaululu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo Yabezi analemekezedwa koposa abale ake; ndi make anamutcha dzina lake Yabezi, ndi kuti, Popeza ndambala mwaululu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Panali munthu wina dzina lake Yabezi amene anthu ankamlemekeza kupambana abale ake. Mai wake pomutcha dzina la Yabezi ankanena kuti, “Chifukwa ndidamubala movutikira.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Yabesi anali munthu wolemekezeka kwambiri kuposa abale ake. Amayi ake anamutcha Yabesi kutanthauza kuti, “Chifukwa ndinamubala ndi ululu wambiri.” Onani mutuwo |