1 Mbiri 4:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo Hakozi anabala Anubu, ndi Zobeba, ndi mabanja a Ahariyele mwana wa Harumu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo Hakozi anabala Anubu, ndi Zobeba, ndi mabanja a Ahariyele mwana wa Harumu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Kozi adabereka Anubu, Zobeba, ndi mabanja a Ahariyele, mwana wa Harumu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 ndi Kozi, amene anali abambo ake a Anubi ndi Hazo-Beba ndi mabanja a Ahariheli mwana wa Harumi. Onani mutuwo |