1 Mbiri 4:6 - Buku Lopatulika6 Ndi Naara anambalira Ahuzamu, ndi Hefere, ndi Temeni, ndi Haahasitari. Iwo ndiwo ana a Naara. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndi Naara anambalira Ahuzamu, ndi Hefere, ndi Temeni, ndi Haahasitari. Iwo ndiwo ana a Naara. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Nara adamubalira Ahuzamu, Hefere, Temeni, ndi Haahasitari. Ameneŵa ndiwo anali ana a Nara. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Naara anamuberekera Ahuzamu, Heferi, Temani ndi Haahasitari. Awa ndiwo anali ana a Naara. Onani mutuwo |