1 Mbiri 4:18 - Buku Lopatulika18 Ndi mkazi wake Myuda anabala Yeredi atate wa Gedori, ndi Hebere atate wa Soko, ndi Yekutiyele atate wa Zanowa. Ndipo awa ndi ana a Bitiya mwana wamkazi wa Farao, amene Meredi anamtenga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndi mkazi wake Myuda anabala Yeredi atate wa Gedori, ndi Hebere atate wa Soko, ndi Yekutiyele atate wa Zanowa. Ndipo awa ndi ana a Bitiya mwana wamkazi wa Farao, amene Meredi anamtenga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Tsono mkazi wake Wachiyuda adamubalira Yeredi, bambo wa Gedori, Hebere bambo wa Soko, ndiponso Yekutiyele bambo wa Zanowa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 (Mkazi wake wa Chiyuda anabereka Yaredi abambo ake a Gedori, Heberi abambo ake a Soko ndi Yekutieli abambo a Zanowa). Awa anali ana a mwana wamkazi wa Farao, Bitia, amene Meredi anakwatira. Onani mutuwo |