Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 4:16 - Buku Lopatulika

16 Ndi ana a Yehalelele: Zifi, ndi Zifa, Tiriya, ndi Asarele.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Ndi ana a Yehalelele: Zifi, ndi Zifa, Tiriya, ndi Asarele.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Ana a Yehalelele naŵa: Zifi, Zifa, Tiriya ndi Asarele.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Ana a Yehaleleli anali awa: Zifi, Zifa, Tiriya ndi Asareli.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 4:16
3 Mawu Ofanana  

Ndi ana a Kalebe mwana wa Yefune: Iru, Ela, ndi Naamu; ndi ana a Ela, ndi Kenazi.


Ndi ana a Ezara: Yetere, ndi Meredi, ndi Efere, ndi Yaloni; ndipo anabala Miriyamu, ndi Samai, ndi Isiba atate wa Esitemowa.


Pamenepo ananyamuka Alevi, Mahati mwana wa Amasai ndi Yowele mwana wa Azariya, a ana a Akohati; ndi a ana a Merari, Kisi mwana wa Abidi, ndi Azariya mwana wa Yehalelele; ndi a Ageresoni, Yowa mwana wa Zima, ndi Edeni mwana wa Yowa;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa