1 Mbiri 4:13 - Buku Lopatulika13 Ndi ana a Kenazi: Otiniyele, ndi Seraya; ndi mwana wa Otiniyele: Hatati. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndi ana a Kenazi: Otiniyele, ndi Seraya; ndi mwana wa Otiniyele: Hatati. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Ana a Kenazi naŵa: Otiniyele ndi Seraya. Ana a Otiniyele naŵa: Hatati ndi Meonotai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Ana a Kenazi anali awa: Otanieli ndi Seraya. Ana a Otanieli anali awa: Hatati ndi Meonotai. Onani mutuwo |