Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 4:12 - Buku Lopatulika

12 Ndi Esitoni, anabala Beterafa, ndi Paseya, ndi Tehina atate wa Irinahasi. Awa ndi anthu a Reka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Ndi Esitoni, anabala Beterafa, ndi Paseya, ndi Tehina atate wa Irinahasi. Awa ndi anthu a Reka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Esitoni adabereka Beterafa, Paseya ndi Tehina, tate wa Irinahasi. Ameneŵa ndiwo anthu a ku Reka.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Esitoni anabereka Beti-Rafa, Paseya ndi Tehina amene anabereka Iri Nahasi. Amenewa ndiwo anthu a ku Reka.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 4:12
2 Mawu Ofanana  

Ndipo Kelubu mbale wa Suha anabala Mehiri, ndiye atate wa Esitoni.


Ndi ana a Kenazi: Otiniyele, ndi Seraya; ndi mwana wa Otiniyele: Hatati.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa