Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 4:11 - Buku Lopatulika

11 Ndipo Kelubu mbale wa Suha anabala Mehiri, ndiye atate wa Esitoni.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo Kelubu mbale wa Suha anabala Mehiri, ndiye atate wa Esitoni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Kelubi, mbale wa Suha, adabereka Meiri, Meiri adabereka Esitoni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Kelubi, mʼbale wa Suha, anabereka Mehiri, amene anabereka Esitoni.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 4:11
2 Mawu Ofanana  

Ndipo Yabezi anaitana kwa Mulungu wa Israele, ndi kuti, Mundidalitse ndithu, ndi kukulitsa malire anga; ndi dzanja lanu likhale ndi ine, nimundisunge, kuti choipa chisandivute. Ndipo Mulungu anafikitsa chopempha iye.


Ndi Esitoni, anabala Beterafa, ndi Paseya, ndi Tehina atate wa Irinahasi. Awa ndi anthu a Reka.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa