Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 3:9 - Buku Lopatulika

9 Onsewa ndiwo ana a Davide, pamodzi ndi ana a akazi aang'ono; ndipo Tamara ndiye mlongo wao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Onsewa ndiwo ana a Davide, pamodzi ndi ana a akazi aang'ono; ndipo Tamara ndiye mlongo wao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Onseŵa anali ana a Davide, osaŵerengera ana a azikazi ake. Mlongo wao anali Tamara.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Onsewa anali ana a Davide, osawerengera ana a azikazi. Ndipo mlongo wawo anali Tamara.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 3:9
5 Mawu Ofanana  

Ndipo Davide anadzitengera akazi aang'ono ena ndi akazi a ulemu ena a ku Yerusalemu, atafikako kuchokera ku Hebroni; ndipo anambadwira Davide ana aamuna ndi aakazi.


ndi mwa ana anga onse (pakuti Yehova wandipatsa ana aamuna ambiri), anasankha Solomoni mwana wanga akhale pa mpando wachifumu wa ufumu wa Yehova kuweruza Israele.


Ndipo mwana wa Solomoni ndiye Rehobowamu, Abiya mwana wake, Asa mwana wake, Yehosafati mwana wake,


ndi Elisama, ndi Eliyada, ndi Elifeleti, asanu ndi anai.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa