Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 3:5 - Buku Lopatulika

5 Ndipo ombadwira mu Yerusalemu ndi awa: Simea, ndi Sobabu, ndi Natani, ndi Solomoni, anai a Batisuwa mwana wamkazi wa Amiyele;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo ombadwira m'Yerusalemu ndi awa: Simea, ndi Sobabu, ndi Natani, ndi Solomoni, anai a Batisuwa mwana wamkazi wa Amiyele;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Ana amene adabadwira ku Yerusalemu ndi aŵa: Simea, Sobabu, Natani ndi Solomoni. Ameneŵa ndiwo ana anai amene adamubalira Batisuwa mwana wa Amiyele.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 ndipo ana amene anabadwira ku Yerusalemuko anali awa: Samua, Sobabu, Natani ndi Solomoni. Ana anayi awa anali a Batisuwa mwana wa Amieli.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 3:5
11 Mawu Ofanana  

Ndipo Davide anatumiza munthu nafunsa za mkaziyo. Ndipo wina anati, Sindiye Bateseba, mwana wamkazi wa Eliyamu, mkazi wa Uriya Muhiti?


Ndipo mfumu Solomoni anayankha, nati kwa amai wake, Mupempheranji Abisagi wa ku Sunamu akhale wake wa Adoniya? Mumpempherenso ufumu, popeza ndiye mkulu wanga; inde ukhale wake, ndi wa Abiyatara wansembeyo, ndi wa Yowabu mwana wa Zeruya.


ndi Ibara, ndi Elisama, ndi Elifeleti,


ndi Yese anabala Davide mfumuyo. Ndipo Davide anabala Solomoni mwa mkazi wa Uriya;


mwana wa Melea, mwana wa Mena, mwana wa Matata, mwana wa Natamu, mwana wa Davide,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa