1 Mbiri 3:16 - Buku Lopatulika16 Ndi ana a Yehoyakimu: Yekoniya mwana wake, Zedekiya mwana wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndi ana a Yehoyakimu: Yekoniya mwana wake, Zedekiya mwana wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Ana aamuna a Yehoyakimu anali aŵa: Yekoniya ndi Zedekiya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ana a Yehoyakimu: Yekoniya ndi Zedekiya mwana wake. Onani mutuwo |
Ndipo kunali chaka cha makumi atatu mphambu zisanu ndi ziwiri cha kumtenga ndende Yehoyakini mfumu ya Yuda, mwezi wakhumi ndi ziwiri, tsiku la makumi awiri mphambu asanu ndi awiri la mwezi, Evili-Merodaki mfumu ya Babiloni anamuweramutsa mutu wake wa Yehoyakini mfumu ya Yuda atuluke m'kaidi, chaka cholowa iye ufumu wake;