Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 3:12 - Buku Lopatulika

12 Amaziya mwana wake, Azariya mwana wake, Yotamu mwana wake,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Amaziya mwana wake, Azariya mwana wake, Yotamu mwana wake,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Yowasi adabereka Amaziya, Amaziya adabereka Azariya, Azariya adabereka Yotamu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Yowasi anabereka Amaziya, Amaziya anabereka Azariya, Azariya anabereka Yotamu,

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 3:12
12 Mawu Ofanana  

Chaka chachiwiri cha Yehowasi mwana wa Yehowahazi mfumu ya Israele, Amaziya mwana wa Yowasi mfumu ya Yuda analowa ufumu wake.


Ndipo anthu onse a Yuda anatenga Azariya, (ndiye Uziya), ndiye wa zaka khumi mphambu zisanu ndi chimodzi, namlonga ufumu m'malo mwa atate wake Amaziya.


Ndipo Hoseya mwana wa Ela anamchitira chiwembu Peka mwana wa Remaliya, namkantha, namupha, nakhala mfumu m'malo mwake chaka cha makumi awiri cha Yotamu mwana wa Uziya.


Chaka chachiwiri cha Peka mwana wa Remaliya mfumu ya Israele, Yotamu mwana wa Uziya mfumu ya Yuda analowa ufumu wake.


Ndipo Yehova anadwaza mfumu, nakhala iye wakhate mpaka tsiku la imfa yake, nakhala m'nyumba ya padera. Ndipo Yotamu mwana wa mfumu anayang'anira banja la mfumu, naweruza anthu a m'dziko.


Nagona Azariya ndi makolo ake, namuika ndi makolo ake m'mzinda wa Davide; nakhala mfumu m'malo mwake Yotamu mwana wake.


Yoramu mwana wake, Ahaziya mwana wake, Yowasi mwana wake,


Ahazi mwana wake, Hezekiya mwana wake, Manase mwana wake,


Amaziya anali wa zaka makumi awiri mphambu zisanu polowa ufumu wake, nakhala mfumu mu Yerusalemu zaka makumi awiri mphambu zisanu ndi zinai; ndi dzina la make ndiye Yehowadani wa ku Yerusalemu.


Ndipo anthu onse Ayuda anatenga Uziya, ndiye wa zaka khumi mphambu zisanu ndi chimodzi, namlonga ufumu m'malo mwa atate wake Amaziya.


Yotamu anali wa zaka makumi awiri, mphambu zisanu polowa ufumu wake, nakhala mfumu mu Yerusalemu zaka khumi ndi zisanu ndi chimodzi; ndi dzina la make ndiye Yerusa mwana wa Zadoki.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa