1 Mbiri 27:4 - Buku Lopatulika4 Woyang'anira chigawo cha mwezi wachiwiri ndiye Dodai Mwahohi ndi chigawo chake; ndi Mikiloti mtsogoleri, ndi m'chigawo chake munali zikwi makumi awiri mphambu zinai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Woyang'anira chigawo cha mwezi wachiwiri ndiye Dodai Mwahohi ndi chigawo chake; ndi Mikiloti mtsogoleri, ndi m'chigawo chake munali zikwi makumi awiri mphambu zinai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Dodai Mwahohi anali woyang'anira gulu la mwezi wachiŵiri. Mtsogoleri wa gulu limeneli anali Mikiloti. Pa gulu lake panali asilikali 24,000. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Amene amalamulira gulu lachiwiri pa mwezi wachiwiri anali Dodai Mwahohi; Mikiloti ndiye anali mtsogoleri wa gulu lake. Pa gulu lake panali asilikali 24,000. Onani mutuwo |