Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 27:34 - Buku Lopatulika

34 ndi wotsatana ndi Ahitofele, Yehoyada mwana wa Benaya, ndi Abiyatara; koma kazembe wa nkhondo ya mfumu ndiye Yowabu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

34 ndi wotsatana ndi Ahitofele, Yehoyada mwana wa Benaya, ndi Abiyatara; koma kazembe wa nkhondo ya mfumu ndiye Yowabu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

34 Ahitofele atamwalira, m'malo mwake mudaloŵa Yehoyada, mwana wa Benaya, ndiponso Abiyatara. Yowabu ndiye anali mtsogoleri wa gulu lankhondo la mfumu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

34 Ahitofele atamwalira mʼmalo mwake munalowa Yehoyada mwana wa Benaya ndi Abiatara. Yowabu anali mtsogoleri wa gulu lankhondo la mfumu.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 27:34
5 Mawu Ofanana  

Ndipo Benaya mwana wa Yehoyada anayang'anira Akereti ndi Apeleti. Ndipo ana a Davide anali ansembe ake.


Ndipo anapangana ndi Yowabu mwana wa Zeruya, ndi Abiyatara wansembeyo; ndipo amenewo anamtsata Adoniya namthandiza.


Nati Davide, Aliyense woyamba kukantha Ayebusi, yemweyo adzakhala mkulu ndi mtsogoleri. Nayamba kukwerako Yowabu mwana wa Zeruya, nakhala mkulu iyeyu.


Ndipo Yowabu mwana wa Zeruya anayang'anira khamu la nkhondo, ndi Yehosafati mwana wa Ahiludi anali wolemba mbiri.


Kazembe wachitatu wa khamu wa mwezi wachitatu ndiye Benaya mwana wa Yehoyada wansembe wamkulu; ndi m'chigawo mwake munalinso zikwi makumi awiri mphambu zinai.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa