1 Mbiri 27:2 - Buku Lopatulika2 Woyang'anira chigawo choyamba cha mwezi, woyamba ndiye Yasobeamu mwana wa Zabidiele; m'chigawo mwake munali zikwi makumi awiri mphambu zinai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Woyang'anira chigawo choyamba cha mwezi, woyamba ndiye Yasobeamu mwana wa Zabidiele; m'chigawo mwake munali zikwi makumi awiri mphambu zinai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Yosobeamu mwana wa Zabidiele ankayang'anira gulu loyamba pa mwezi woyamba. Pa gulu lake panali asilikali 24,000. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Amene amalamulira gulu loyamba pa mwezi woyamba anali Yasobeamu mwana wa Zabidieli. Pa gulu lake panali asilikali 24,000. Onani mutuwo |
Ndipo ana a Israele monga mwa chiwerengo chao, kunena za akulu a nyumba za makolo ao, ndi akazembe a zikwi, ndi a mazana, ndi akapitao ao akutumikira mfumu mu ntchito iliyonse ya magawidwe, akulowa ndi kutuluka mwezi ndi mwezi, miyezi yonse ya chaka, chigawo chilichonse ncha amuna zikwi makumi awiri mphambu zinai.