1 Mbiri 26:9 - Buku Lopatulika9 Ndi Meselemiya anali ndi ana, ndi abale odziwa mphamvu khumi mphambu asanu ndi atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndi Meselemiya anali ndi ana, ndi abale odziwa mphamvu khumi mphambu asanu ndi atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Kuchokera ku banja la Meselemiya kudasankhidwa anthu aluso 18. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Meselemiya anali ndi ana ndi abale ake amene anali aluso ndipo onse analipo 18. Onani mutuwo |