1 Mbiri 26:8 - Buku Lopatulika8 Onsewa ndiwo a ana a Obededomu; iwo ndi ana ao, ndi abale ao, anthu odziwa mphamvu yakutumikira, makumi asanu ndi limodzi mphambu awiri a Obededomu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Onsewa ndiwo a ana a Obededomu; iwo ndi ana ao, ndi abale ao, anthu odziwa mphamvu yakutumikira, makumi asanu ndi limodzi mphambu awiri a Obededomu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Kuchokera ku banja la Obededomu kudasankhidwa anthu 62, onsewo okhoza ntchito. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Onsewa anali adzukulu a Obedi-Edomu. Iwo ndi ana awo ndiponso abale awo anali anthu aluso ndi amphamvu pogwira ntchito. Zidzukulu zonse za Obedi-Edomu zinalipo 62. Onani mutuwo |