1 Mbiri 26:7 - Buku Lopatulika7 Ana a Semaya: Otini, ndi Refaele, ndi Obedi, Elizabadi, amene abale ao ndiwo odziwa mphamvu, Elihu, ndi Semakiya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ana a Semaya: Otini, ndi Refaele, ndi Obedi, Elizabadi, amene abale ao ndiwo odziwa mphamvu, Elihu, ndi Semakiya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Ana a Semaya naŵa: Otini, Refaele, Obede ndi Elizabadi amene anali ndi abale ao amphamvu, Elihu ndi Semakiya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Ana a Semaya anali: Otini, Refaeli, Obedi ndi Elizabadi; abale ake, Elihu ndi Semakiya, analinso anthu amphamvu. Onani mutuwo |