Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 26:6 - Buku Lopatulika

6 Kwa Semaya mwana wake yemwe kunabadwa ana, akulamulira nyumba ya atate wao; pakuti anali ngwazi zamphamvu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Kwa Semaya mwana wake yemwe kunabadwa ana, akulamulira nyumba ya atate wao; pakuti anali ngwazi zamphamvu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Semaya mwana wake nayenso anali ndi ana amene anali otchuka m'mabanja a makolo ao, makamaka aŵiri omariza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Mwana wake Semaya analinso ndi ana amene anali atsogoleri mʼbanja la abambo awo chifukwa anali anthu amphamvu.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 26:6
10 Mawu Ofanana  

Chifukwa chake tsono manja anu alimbike, nimuchite chamuna; pakuti Saulo mbuye wanu wafa, ndi a nyumba ya Yuda anandidzoza ndikhale mfumu yao.


ndi Zadoki, ndiye mnyamata, ngwazi yamphamvu, ndi a nyumba ya kholo lake akulu makumi awiri mphambu awiri.


wachisanu ndi chimodzi Amiyele, wachisanu ndi chiwiri Isakara, wachisanu ndi chitatu Peuletai; pakuti Mulungu adamdalitsa.


Ana a Semaya: Otini, ndi Refaele, ndi Obedi, Elizabadi, amene abale ao ndiwo odziwa mphamvu, Elihu, ndi Semakiya.


Onsewa ndiwo a ana a Obededomu; iwo ndi ana ao, ndi abale ao, anthu odziwa mphamvu yakutumikira, makumi asanu ndi limodzi mphambu awiri a Obededomu.


Ndipo Azariya wansembe analowa pambuyo pake, ndi pamodzi naye ansembe a Yehova makumi asanu ndi atatu, ndiwo olimba mtima;


ndi abale ao, ngwazi zamphamvu, zana limodzi mphambu makumi awiri kudza asanu ndi atatu; ndi woyang'anira wao ndiye Zabidiele mwana wa Hagedolimu.


Limba nayo nkhondo yabwino ya chikhulupiriro, gwira moyo wosatha, umene adakuitanira, ndipo wavomereza chivomerezo chabwino pamaso pa mboni zambiri.


Umve zowawa pamodzi nane monga msilikali wabwino wa Khristu Yesu.


Ndipo mthenga wa Yehova anamuonekera, nati kwa iye, Yehova ali nawe, ngwazi iwe, wamphamvu iwe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa