Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 26:5 - Buku Lopatulika

5 wachisanu ndi chimodzi Amiyele, wachisanu ndi chiwiri Isakara, wachisanu ndi chitatu Peuletai; pakuti Mulungu adamdalitsa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 wachisanu ndi chimodzi Amiyele, wachisanu ndi chiwiri Isakara, wachisanu ndi chitatu Peuletai; pakuti Mulungu adamdalitsa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 wachisanu ndi chimodzi Amiyele, wachisanu ndi chiŵiri Isakara ndipo wachisanu ndi chitatu Peuletai, (pakuti paja Mulungu adaamdalitsa Obededomuyo.)

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 wachisanu ndi chimodzi Amieli, wachisanu ndi chiwiri Isakara ndipo wachisanu ndi chitatu Peuletayi. (Pakuti Mulungu anadalitsa Obedi-Edomu).

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 26:5
5 Mawu Ofanana  

Pamenepo anthu anauza mfumu Davide, kuti Yehova wadalitsa banja la Obededomu ndi zake zonse, chifukwa cha likasa la Mulungu. Chomwecho Davide anamuka nakatenga likasa la Mulungu kunyumba ya Obededomu, nakwera nalo kumzinda wa Davide, ali ndi chimwemwe.


Ndi likasa la Mulungu linakhala ndi banja la Obededomu m'nyumba mwake miyezi itatu; ndipo Yehova anadalitsa nyumba ya Obededomu, ndi zonse anali nazo.


Ndipo Obededomu anali nao ana, woyamba Semaya, wachiwiri Yehozabadi, wachitatu Yowa, wachinai Sakara, wachisanu Netanele,


Kwa Semaya mwana wake yemwe kunabadwa ana, akulamulira nyumba ya atate wao; pakuti anali ngwazi zamphamvu.


Wodala yense wakuopa Yehova, wakuyenda m'njira zake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa