1 Mbiri 26:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo Meselemiya anali ndi ana, woyamba Zekariya, wachiwiri Yediyaele, wachitatu Zebadiya, wachinai Yatiniele, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Meselemiya anali ndi ana, woyamba Zekariya, wachiwiri Yediyaele, wachitatu Zebadiya, wachinai Yatiniele, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Meselemiya anali ndi ana aŵa: wachisamba anali Zekariya, wachiŵiri Yediyale, wachitatu Zebadiya, wachinai Yatiniele, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Meselemiya anali ndi ana awa: woyamba Zekariya, wachiwiri Yediaeli, wachitatu Zebadiya, wachinayi Yatinieli, Onani mutuwo |