Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Mbiri 26:18 - Buku Lopatulika

18 Ku Parabara kumadzulo anai kumseu, ndi awiri ku Parabara.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Ku Parabara kumadzulo anai kumseu, ndi awiri ku Parabara.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Ku bwalo lakuzambwe kunali alonda anai ku mseu ndiponso alonda aŵiri ku bwalo lenilenilo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Ndipo ku bwalo cha kumadzulo, anayi amakhala mu msewu ndi awiri pabwalo penipeni.

Onani mutuwo Koperani




1 Mbiri 26:18
4 Mawu Ofanana  

Nachotsanso akavalo amene mafumu a Yuda adapereka kwa dzuwa, polowera nyumba ya Yehova, ku chipinda cha Natani-Meleki mdindoyo, chokhala kukhonde; natentha magaleta a dzuwa ndi moto.


Supimu ndi Hosa kumadzulo, ku chipata cha Saleketi, ku mseu wokwerapo, udikiro pandunji pa udikiro.


Kum'mawa kunali Alevi asanu ndi mmodzi, kumpoto anai tsiku ndi tsiku, kumwera anai tsiku ndi tsiku, ndi a nyumba ya akatundu awiri ndi awiri.


Awa ndi magawidwe a odikira; a ana a Akora, ndi a ana a Merari.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa