1 Mbiri 26:16 - Buku Lopatulika16 Supimu ndi Hosa kumadzulo, ku chipata cha Saleketi, ku mseu wokwerapo, udikiro pandunji pa udikiro. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Supimu ndi Hosa kumadzulo, ku chipata cha Saleketi, ku mseu wokwerapo, udikiro pandunji pa udikiro. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Supimu ndi Hosa adaŵasankha kuti azilonda kuzambwe ku khomo la Saleketi, pa mseu wokwera. Maulonda ankakhala otsatanatsatana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Maere a chipata chakumadzulo ndi chipata cha Saleketi ku msewu wa ku mtunda anagwera Supimu ndi Hosa. Mlonda ankayangʼanana ndi mlonda mnzake: Onani mutuwo |