1 Mbiri 26:14 - Buku Lopatulika14 Ndi maere a kum'mawa anagwera Selemiya. Ndipo anachitira maere Zekariya mwana wake, phungu wanzeru, ndi maere anamgwera kumpoto; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndi maere a kum'mawa anagwera Selemiya. Ndipo anachitira maere Zekariya mwana wake, phungu wanzeru, ndi maere anamgwera kumpoto; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Selemiya adamsankha kuti azilonda pa khomo lakuvuma. Mwana wake Zekariya, phungu wanzeru, adamsankha kuti azilonda khomo lakumpoto. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Maere a chipata chakummwa anagwera Selemiya. Maere anachitikanso chifukwa cha mwana wake Zekariya, phungu wanzeru ndipo maere a chipata chakumpoto anagwera iye. Onani mutuwo |