1 Mbiri 26:12 - Buku Lopatulika12 Mwa iwowa munali magawidwe a odikira, mwa akulu a amuna akuchita udikiro wao, monga abale ao, kutumikira m'nyumba ya Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Mwa iwowa munali magawidwe a odikira, mwa akulu a amuna akuchita udikiro wao, monga abale ao, kutumikira m'nyumba ya Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Alonda a pa khomo la Nyumba ya Chauta adaŵaika m'magulu, potsata mabanja ao, ndipo adaŵapatsa ntchito zao zotumikira, monga momwe adachitira Alevi anzao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Magulu amenewa a alonda a pa zipata, motsogozedwa ndi atsogoleri awo, anali ndi ntchito yotumikira mʼNyumba ya Yehova, monga momwe amachitira abale awo. Onani mutuwo |