1 Mbiri 26:11 - Buku Lopatulika11 wachiwiri Hilikiya, wachitatu Tebaliya, wachinai Zekariya; ana ndi abale onse a Hosa ndiwo khumi ndi atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 wachiwiri Hilikiya, wachitatu Tebaliya, wachinai Zekariya; ana ndi abale onse a Hosa ndiwo khumi ndi atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Wachiŵiri Hilikiya, wachitatu Tebaliya, wachinai anali Zekariya. Onse a m'banja la Hosa amene anali alonda analipo 13. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 wachiwiri Hilikiya, wachitatu Tebaliya ndipo wachinayi Zekariya. Ana ndi abale onse a Hosa analipo 13. Onani mutuwo |