1 Mbiri 26:10 - Buku Lopatulika10 Hosa yemwe wa ana a Merari anali ndi ana, wamkulu ndi Simiri; pakuti ngakhale sanali wobadwa woyamba, atate wake anamuyesa wamkulu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Hosa yemwe wa ana a Merari anali ndi ana, wamkulu ndi Simiri; pakuti ngakhale sanali wobadwa woyamba, atate wake anamuyesa wamkulu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Kuchokera ku banja la Merari kudasankhidwa Hosa amene anali ndi ana aŵa: Simiri mtsogoleri (iyeyu ngakhale sanali mwana wachisamba, atate ake adaamsankhula kuti akhale mtsogoleri.) Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Hosa Mmerari anali ndi ana awa: woyamba anali Simiri (ngakhale kuti iye sanali woyamba kubadwa, abambo ake anamusankha kuti akhale mtsogoleri), Onani mutuwo |