1 Mbiri 24:2 - Buku Lopatulika2 Koma Nadabu ndi Abihu anafa, atate wao akali ndi moyo, opanda ana; momwemo Eleazara ndi Itamara anachita ntchito ya nsembe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Koma Nadabu ndi Abihu anafa, atate wao akali ndi moyo, opanda ana; momwemo Eleazara ndi Itamara anachita ntchito ya nsembe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Koma Nadabu ndi Abihu adafa bambo wao akali moyo, ndipo analibe ana. Motero Eleazara ndi Itamara adaloŵa unsembe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Koma Nadabu ndi Abihu anamwalira abambo awo asanamwalire, ndipo analibe ana aamuna. Kotero Eliezara ndi Itamara ankatumikira monga ansembe. Onani mutuwo |