1 Mbiri 23:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo anawerengedwa Alevi oyambira zaka makumi atatu ndi mphambu, ndipo chiwerengo chao kuwawerenga mmodzimmodzi ndicho amuna zikwi makumi atatu mphambu zisanu ndi zitatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo anawerengedwa Alevi oyambira zaka makumi atatu ndi mphambu, ndipo chiwerengo chao kuwawerenga mmodzimmodzi ndicho amuna zikwi makumi atatu mphambu zisanu ndi zitatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Adaŵerenga Aleviwo kuyambira a zaka makumi atatu ndi kupitirirapo. Chiŵerengero chao chinali anthu 38,000. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Anawerenga Alevi kuyambira a zaka makumi atatu ndi kupitirirapo, ndipo chiwerengero cha amuna onse chinali 38,000. Onani mutuwo |