1 Mbiri 23:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo anasonkhanitsa akulu onse a Israele, ndi ansembe ndi Alevi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo anasonkhanitsa akulu onse a Israele, ndi ansembe ndi Alevi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Davide adasonkhanitsa atsogoleri onse a Israele, ansembe ndi Alevi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iye anasonkhanitsanso pamodzi atsogoleri onse a Israeli, pamodzi ndi ansembe ndi Alevi. Onani mutuwo |
Pamenepo Davide anasonkhanitsa ku Yerusalemu akalonga a Israele, akalonga a mafuko, ndi akulu a zigawo zakutumikira mfumu, ndi akulu a zikwi, ndi akulu a mazana, ndi akulu a zolemera zonse, ndi zoweta zonse za mfumu, ndi ana ake; pamodzi ndi akapitao ndi anthu amphamvu, ndiwo ngwazi zamphamvu onsewo.