1 Mbiri 22:4 - Buku Lopatulika4 ndi mitengo yamikungudza yosaiwerenga; pakuti Asidoni ndi Atiro anabwera nayo kwa Davide mitengo yamikungudza yochuluka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 ndi mitengo yamikungudza yosaiwerenga; pakuti Asidoni ndi Atiro anabwera nayo kwa Davide mitengo yamikungudza yochuluka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Adaperekanso matabwa osaŵerengeka a mtengo wa mkungudza, chifukwa anthu a ku Sidoni ndi a ku Tiro adaabwera ndi mikungudza yambiri kwa Davide. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Iye anaperekanso mitengo yambiri ya mkungudza, yosawerengeka, pakuti anthu a ku Sidoni ndi a ku Turo anabweretsa yambiri kwa Davide. Onani mutuwo |